Genesis 32:23 - Buku Lopatulika23 Ndipo anawatenga iwo nawaolotsa pamtsinje, naziolotsa zonse anali nazo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Ndipo anawatenga iwo nawaolotsa pamtsinje, naziolotsa zonse anali nazo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Ataŵaolotsa onse aja, adaolotsanso chuma chake chonse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Atatha kuwawolotsa pa mtsinjewo anawolotsanso katundu wake yense. Onani mutuwo |