Genesis 32:21 - Buku Lopatulika21 Momwemo naolotsa mphatso patsogolo pake: ndipo iye yekha anagona usiku womwewo pachigono. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Momwemo naolotsa mphatso patsogolo pake: ndipo iye yekha anagona usiku womwewo pachigono. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Choncho mphatsozo zidatsogola, ndipo usiku umenewo Yakobe adagona kumahema konkuja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Choncho mphatso za Yakobo zinatsogola, koma iye mwini anagona pa msasa pomwepo usiku umenewo. Onani mutuwo |