Genesis 32:13 - Buku Lopatulika13 Ndipo anagona komweko usiku womwewo, natengako zimene anali nazo, mphatso yakupatsa Esau mkulu wake: Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Ndipo anagona komweko usiku womwewo, natengako zimene anali nazo, mphatso yakupatsa Esau mkulu wake: Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Atagona kumeneko, pambuyo pake adasankhula mphatso izi pa chuma chonse chimene anali nacho: Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Iye anagona pomwepo usiku umenewo. Pambuyo pake anasankhula pa chuma chimene anali nacho zinthu izi ngati mphatso za Esau, mʼbale wake: Onani mutuwo |