Genesis 30:4 - Buku Lopatulika4 Ndipo Rakele anampatsa iye Biliha mdzakazi wake akhale mkazi wake; ndipo Yakobo analowa kwa iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ndipo Rakele anampatsa iye Biliha mdzakazi wake akhale mkazi wake; ndipo Yakobo analowa kwa iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Choncho Rakele adapereka Biliha kwa mwamuna wake, ndipo adakhala naye. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Ndipo anamupatsa Yakobo wantchito wake Biliha kuti alowane naye. Choncho Yakobo analowana ndi Biliha, Onani mutuwo |