Genesis 30:39 - Buku Lopatulika39 Ndipo ziweto zinatenga mabere patsogolo pa nthyolezo, ndipo zoweta zinabala zamipyololomipyololo, ndi mathothomathotho, ndi zamawangamawanga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201439 Ndipo ziweto zinatenga mabere patsogolo pa nthyolezo, ndipo zoweta zinabala zamipyololomipyololo, ndi mathothomathotho, ndi zamawangamawanga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa39 Motero zoŵetazo zikatenga maŵere zitayang'ana nthambizo, ana ake ankakhala ndi maonekedwe amathothomathotho ndiponso amaŵangamaŵanga. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero39 Ndiye kuti nkhosa zija zinkatenga mawere pakumwa madzi molunjika nthambi zija, ndipo zinkaswa ana a mawangamawanga kapena a mathothomathotho. Onani mutuwo |