Genesis 30:29 - Buku Lopatulika29 Ndipo iye anati kwa Labani, Udziwa iwe chomwe ndakutumikira iwe ndi chomwe zachita zoweta zako ndi ine. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201429 Ndipo iye anati kwa Labani, Udziwa iwe chomwe ndakutumikira iwe ndi chomwe zachita zoweta zako ndi ine. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa29 Yakobe adayankha kuti, “Mukudziŵa m'mene ndakugwirirani ntchito, ndi m'mene zoŵeta zanu zaswanirana kwambiri pozisamala ine. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero29 Koma Yakobo anati kwa iye, “Inu mukudziwa mmene ine ndakugwirirani ntchito ndi mmene ziweto zanu zaswanira pamene ine ndimazisamalira. Onani mutuwo |