Genesis 30:2 - Buku Lopatulika2 Ndipo Yakobo anapsa mtima ndi Rakele; nati, Kodi ine ndikhala m'malo a Mulungu amene akukaniza iwe zipatso za mimba? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndipo Yakobo anapsa mtima ndi Rakele; nati, Kodi ine ndikhala m'malo a Mulungu amene akukaniza iwe zipatso za mimba? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Yakobe adapsera mtima Rakele, namuuza kuti, “Sindingathe kuloŵa m'malo mwa Mulungu. Iyeyo ndiye akukuletsa kubala ana.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Yakobo anapsera mtima Rakele ndipo nati, “Kodi ine ndalowa mʼmalo mwa Mulungu amene wakulepheretsa iwe kukhala ndi ana?” Onani mutuwo |