Genesis 30:19 - Buku Lopatulika19 Ndipo Leya anatenganso pakati nambalira Yakobo mwana wamwamuna wachisanu ndi chimodzi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Ndipo Leya anatenganso pakati nambalira Yakobo mwana wamwamuna wachisanu ndi chimodzi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Leya adatenganso pena pathupi, namubalira Yakobe mwana wamwamuna wachisanu ndi chimodzi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Leya anatenganso pathupi nabalira Yakobo mwana wa mwamuna wachisanu ndi chimodzi. Onani mutuwo |