Genesis 3:11 - Buku Lopatulika11 Ndipo anati, Ndani anakuuza iwe kuti uli wamaliseche? Kodi wadya za mtengo uja, umene ndinakuuza iwe kuti usadye? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Ndipo anati, Ndani anakuuza iwe kuti uli wamaliseche? Kodi wadya za mtengo uja, umene ndinakuuza iwe kuti usadye? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Mulungu adamufunsa kuti, “Kodi adakuuza ndani kuti uli maliseche? Kapena wadyatu zipatso za mtengo uja ndidakuuza kuti usadyewu eti?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Ndipo anamufunsa, “Ndani anakuwuza kuti uli maliseche? Kodi wadya zipatso za mtengo umene ndinakulamulira kuti usadye?” Onani mutuwo |