Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 28:8 - Buku Lopatulika

8 ndipo Esau anaona kuti ana aakazi a Kanani sanakondweretse Isaki atate wake:

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 ndipo Esau anaona kuti ana akazi a Kanani sanakondweretsa Isaki atate wake:

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Pamenepo Esau adadziŵa kuti bambo wake Isaki sankaŵakonda akazi a ku Kanani.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 Ndiye pamenepo Esau anazindikira kuti abambo ake Isake sankakondwera ndi akazi a ku Kanaani;

Onani mutuwo Koperani




Genesis 28:8
6 Mawu Ofanana  

ndipo ndidzakulumbiritsa iwe pa Yehova, Mulungu wa Kumwamba, ndi Mulungu wa dziko lapansi, kuti usadzamtengere mwana wanga mkazi wa kwa ana aakazi a Akananiwo, amene ndikhala pakati pao.


Ndipo anati Rebeka kwa Isaki, Ndalema moyo wanga chifukwa cha ana aakazi a Ahiti, akatenga Yakobo mkazi wa ana aakazi a Ahiti, onga ana aakazi a m'dziko lino, moyo wanga udzandikhalira ine bwanji?


Ndipo Isaki anamuitana Yakobo, namdalitsa iye, namuuza iye, nati kwa iye, Usatenge mkazi wa ana aakazi a Kanani.


ndiponso kuti Yakobo anamvera atate wake ndi amake, nanka ku Padanaramu;


Koma chimenechi sichinakondweretse Samuele, pamene iwo anati, Tipatseni mfumu kuti itiweruze. Ndipo Samuele anapemphera kwa Yehova.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa