Genesis 28:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo Isaki anamuitana Yakobo, namdalitsa iye, namuuza iye, nati kwa iye, Usatenge mkazi wa ana aakazi a Kanani. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo Isaki anamuitana Yakobo, namdalitsa iye, namuuza iye, nati kwa iye, Usatenge mkazi wa ana akazi a Kanani. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Pamenepo Isaki adaitana Yakobe namdalitsa, ndipo adamlamula kuti, “Usakwatire mkazi wa kuno ku Kanani. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Choncho Isake anayitanitsa Yakobo namudalitsa nʼkumuwuzitsa kuti, “Usakwatire mkazi wa kuno ku Kanaani. Onani mutuwo |