Genesis 27:24 - Buku Lopatulika24 Ndipo anati, Kodi ndiwe mwana wanga weniweni Esau? Ndipo anati, Ndine amene. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 Ndipo anati, Kodi ndiwe mwana wanga weniweni Esau? Ndipo anati, Ndine amene. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 Koma adafunsanso kuti, “Kodi ndiwedi mwana wanga Esau?” Yakobe adayankhanso kuti, “Ndine amene.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 Isake anafunsa, “Kodi ndiwedi mwana wanga Esau?” Yakobo anayankha, “Inde ndine.” Onani mutuwo |