Genesis 27:23 - Buku Lopatulika23 Ndipo sanamzindikire iye, chifukwa kuti manja ake anali aubweya, onga manja a Esau mkulu wake; ndipo anamdalitsa iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Ndipo sanamzindikire iye, chifukwa kuti manja ake anali aubweya, onga manja a Esau mkulu wake; ndipo anamdalitsa iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Sadamzindikire Yakobe popeza kuti mikono yake inali yacheya ngati ya Esau. Motero adayambapo kumdalitsa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Sanamuzindikire, popeza mikono yake inali ndi ubweya ngati ya mʼbale wake Esau; choncho anamudalitsa. Onani mutuwo |