Genesis 27:21 - Buku Lopatulika21 Ndipo Isaki anati kwa Yakobo, Sendera kuno, ndikuyambase mwana wanga, ngati ndiwe mwana wanga Esau ndithu, kapena wina. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Ndipo Isaki anati kwa Yakobo, Sendera kuno, ndikuyambase mwana wanga, ngati ndiwe mwana wanga Esau ndithu, kapena wina. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Isaki adauza Yakobe kuti, “Tasendera pafupi kuti ndikukhudze, kuti ndidziŵe ngati ndiwedi mwana wanga Esau, kapena ai.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Pamenepo Isake anati kwa Yakobo, “Tabwera pafupi ndikukhudze mwana wanga, kuti ndidziwedi ngati uli mwana wanga Esau kapena ayi.” Onani mutuwo |