Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 25:4 - Buku Lopatulika

4 Ana a Midiyani: Efa, ndi Efere, ndi Hanoki, ndi Abida, ndi Elida. Onse amenewa ndi ana a Ketura.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

4 Ana a Midiyani: Efa, ndi Efere, ndi Hanoki, ndi Abida, ndi Elida. Onse amenewa ndi ana a Ketura.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

4 Ana a Midiyani anali Efa, Efera, Hanoki, Abida ndi Elida. Onseŵa anali zidzukulu za Ketura.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

4 Ana aamuna a Midiyani anali, Efai, Eferi, Hanoki, Abida ndi Elida. Onsewa anali zidzukulu za Ketura.

Onani mutuwo Koperani




Genesis 25:4
5 Mawu Ofanana  

Ndipo Yokisani anabala Sheba, ndi Dedani. Ana a Dedani ndi Aasuri, ndi Aletusi, ndi Aleumi.


Ndipo Abrahamu anampatsa Isaki zonse anali nazo.


Ndipo anachoka ku Midiyani nafika ku Parani, natenga anthu a ku Parani pamodzi nao, nafika ku Ejipito kwa Farao mfumu ya Aejipito, ameneyo anampatsa nyumba, namnenera zakudya, nampatsako dziko.


Ndi ana a Midiyani: Efa, ndi Efere, ndi Hanoki, ndi Abida, ndi Elida. Awa onse ndiwo ana a Ketura.


Gulu la ngamira lidzakukuta, ngamira zazing'ono za Midiyani ndi Efa; iwo onsewo adzachokera ku Sheba adzabwera nazo golide ndi lubani; ndipo adzalalikira matamando a Yehova.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa