Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 25:10 - Buku Lopatulika

10 munda umene anagula Abrahamu kwa ana a Hiti. Pamenepo anamuika Abrahamu ndi Sara mkazi wake.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

10 munda umene anagula Abrahamu kwa ana a Hiti: pamenepo anamuika Abrahamu ndi Sara mkazi wake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

10 Unali munda umene Abrahamu adaagula kwa Ahiti. Abrahamu ndi mkazi wake Sara adaikidwa kumeneko.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

10 uwu ndi munda umene Abrahamu anagula kwa Ahiti. Kumeneko Abrahamu anakayikidwa pamodzi ndi mkazi wake Sara.

Onani mutuwo Koperani




Genesis 25:10
8 Mawu Ofanana  

Ndipo Kanani anabala Sidoni woyamba wake, ndi Heti,


Ndipo Abrahamu anamvera Efuroni, ndipo Abrahamu anamuyesera Efuroni ndalama zimene ananena alinkumva ana a Hiti, masekeli a siliva mazana anai, ndalama zomwezo agulana nazo malonda.


Ndipo munda wa Efuroni umene unali mu Makipela, umene unali patsogolo pa Mamure, munda ndi phanga lili momwemo, ndi mitengo yonse inali m'mundamo, yokhala m'malire monse mozungulira momwemo,


Ndipo ana a Hiti analimbitsira Abrahamu munda, ndi phanga lili m'menemo, likhale lake lamanda.


Ndipo Abrahamu anauka pa wakufa wake, nanena kwa ana a Hiti, nati,


kuti andipatse ine phanga la Makipela, limene lili pansonga pamunda wake; pa mtengo wake wonse andipatse pakati pa inu, ndikhale nao manda.


koma pamene ndidzagona ndi makolo anga, udzanditenge ine kutuluka m'dziko la Ejipito, ukandiike ine m'manda mwao. Ndipo iye anati, Ndidzachita monga mwanena.


pamenepo anaika Abrahamu ndi Sara mkazi wake; pamenepo anaika Isaki ndi Rebeka mkazi wake: pamenepo ndinaika Leya:


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa