Genesis 24:62 - Buku Lopatulika62 Ndipo Isaki anadzera njira ya Beere-Lahai-Roi; chifukwa kuti anakhala iye m'dziko la kumwera. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201462 Ndipo Isaki anadzera njira ya Beere-Lahai-Roi; chifukwa kuti anakhala iye m'dziko la kumwera. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa62 Isaki anali atachoka kuchipululu kumene kunali chitsime cha Wamoyo-Wondipenya chija, kukakhala m'chigawo chakumwera. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero62 Pa nthawiyi nʼkuti Isake atafika kuchokera ku chitsime cha Wamoyo Wondipenya (Beeri-lahai-roi), popeza tsopano ankakhala ku Negevi. Onani mutuwo |