Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Genesis 24:63 - Buku Lopatulika

63 Ndipo Isaki anatuluka kulingalira m'munda madzulo; ndipo anatukula maso ake, nayang'ana, taona, ngamira zinalinkudza.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

63 Ndipo Isaki anatuluka kulingalira m'munda madzulo; ndipo anatukula maso ake, nayang'ana, taona, ngamira zinalinkudza.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

63 Tsiku lina madzulo, Isakiyo ankapita nayenda kuthengo, ndipo adaona ngamira zilikudza.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

63 Tsiku lina chakumadzulo, Isake anatuluka kukayendayenda ku munda, ndipo atakweza maso anaona ngamira zikubwera.

Onani mutuwo Koperani




Genesis 24:63
12 Mawu Ofanana  

Ndipo anatukula maso ake, nayang'ana, taonani, anthu atatu anaima pandunji pake; pamene anaona iwo, anawathamangira kuchoka ku khomo la hema kukakomana nao, nawerama pansi, nati,


Ndipo Rebeka anatukula maso ake, ndipo pamene anaona Isaki anatsika pa ngamira.


Komatu m'chilamulo cha Yehova muli chikondwerero chake; ndipo m'chilamulo chake amalingirira usana ndi usiku.


Pomlingirira Iye pandikonde; ndidzakondwera mwa Yehova.


Ndidzalingirira pa malangizo anu, ndi kupenyerera mayendedwe anu.


Mundizindikiritse njira ya malangizo anu; kuti ndilingalire zodabwitsa zanu.


Ndidzakwezanso manja anga ku malamulo anu, amene ndiwakonda; ndipo ndidzalingalira pa malemba anu.


Ndidzalingalira ulemerero waukulu wa ulemu wanu, ndi ntchito zanu zodabwitsa.


Buku ili la chilamulo lisachoke pakamwa pako; koma ulingiriremo usana ndi usiku, kuti usamalire kuchita monga mwa zonse zolembedwamo; popeza ukatero udzakometsa njira yako, nudzachita mwanzeru.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa