Genesis 24:57 - Buku Lopatulika57 Ndipo anati iwo, Tidzamuitana namwaliyo, tidzamfunsa pakamwa pake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201457 Ndipo anati iwo, Tidzamuitana namwaliyo, tidzamfunsa pakamwa pake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa57 Apo iwowo adayankha kuti, “Tiyeni timuitane namwaliyo, kuti timve zimene iyeyo anene.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero57 Koma iwo anati, “Bwanji timuyitane mtsikanayo ndipo timufunse ngati afuna kupita nanu panopa.” Onani mutuwo |