Genesis 24:58 - Buku Lopatulika58 Ndipo anamuitana Rebeka nati kwa iye, Kodi udzanka pamodzi ndi munthuyo? Ndipo anati, Ndidzanka. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201458 Ndipo anamuitana Rebeka nati kwa iye, Kodi udzanka pamodzi ndi munthuyo? Ndipo anati, Ndidzanka. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa58 Motero adamuitana Rebeka namufunsa kuti, “Kodi ukufuna kupita naye munthuyu?” Rebekayo adayankha kuti, “Inde, ndipita.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero58 Choncho iwo anamuyitana Rebeka uja namufunsa kuti, “Kodi ukufuna kupita ndi munthuyu panopa?” Iye anayankha kuti, “Ndipita.” Onani mutuwo |