Genesis 24:51 - Buku Lopatulika51 Taonani, Rebeka ali pamaso pako, mtenge ndi kumuka, akhale mkazi wa mwana wa mbuyako, monga wanena Yehova. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201451 Taonani, Rebeka ali pamaso pako, mtenge ndi kumuka, akhale mkazi wa mwana wa mbuyako, monga wanena Yehova. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa51 Nayu, Rebeka ndi ameneyu, mtengeni muzipita naye. Mukampereke kwa mwana wa mbuyanuyo kuti akakhale mkazi wake, monga momwe Chauta adanenera.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero51 Nayu Rebeka, mutengeni muzipita naye kuti akakhale mkazi wa mwana wa mbuye wanu, monga Yehova wanenera.” Onani mutuwo |