Genesis 24:46 - Buku Lopatulika46 Ndipo iye anafulumira, natsitsa mtsuko pa phewa lake, nati, Imwatu, ndipo ndidzamwetsanso ngamira zako: ndipo ndinamwa, ndipo anamwetsa ngamira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201446 Ndipo iye anafulumira, natsitsa mtsuko pa phewa lake, nati, Imwatu, ndipo ndidzamwetsanso ngamira zako: ndipo ndinamwa, ndipo anamwetsa ngamira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa46 Mosachedwa anatsitsa mtsuko wake pa phewa, nandiwuza kuti, ‘Imwani, ndipo ndimwetsanso ngamira zanuzi.’ Motero ine ndinamwa, ndipo iye anamwetsanso ngamirazo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero46 “Mofulumira, anatsitsa mtsuko wake pa phewa pake nati, ‘Imwani ndiponso ndizimwetsa madzi ngamira zanuzi.’ Kotero ine ndinamwa ndipo anamwetsanso ngamirazo. Onani mutuwo |