Genesis 24:4 - Buku Lopatulika4 Koma udzanke ku dziko langa, kwa abale anga, ndi kumtengera mwana wanga Isaki mkazi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Koma udzanke ku dziko langa, kwa abale anga, ndi kumtengera mwana wanga Isaki mkazi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Koma udzapita ku dziko lakwathu, ndipo ukamutengera mkazi mwana wanga kumeneko pakati pa abale anga.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 koma kuti udzapita ku dziko la kwathu ndi kukamupezera mkazi mwana wanga Isake pakati pa abale anga.” Onani mutuwo |