Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 24:13 - Buku Lopatulika

13 Taonani, ine ndiima pa chitsime cha madzi; ndipo ana aakazi a m'mzinda atuluka kudzatunga madzi;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

13 Taonani, ine ndiima pa chitsime cha madzi; ndipo ana akazi a m'mudzi atuluka kudzatunga madzi;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

13 Ndili pano pa chitsime, ndipo akazi amumzindamu abwera kudzatunga madzi.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

13 Taonani ndayima pambali pa chitsimechi, ndipo atsikana a mu mzindawu akubwera kudzatunga madzi.

Onani mutuwo Koperani




Genesis 24:13
10 Mawu Ofanana  

Ndipo anagwaditsa ngamira zake kunja kwa mzinda, ku chitsime cha madzi nthawi yamadzulo, nthawi yotuluka akazi kudzatunga madzi.


ndipo pakhale kuti namwali amene ndidzati kwa iye, Tulatu mtsuko wako, ndimwe; ndipo iye adzati, Imwa, ndipo ndidzamwetsanso ngamira zako; yemweyo akhale mkazi wosankhira mnyamata wanu Isaki; ndipo chotero ndidzadziwa kuti mwamchitira mbuyanga ufulu.


taonani, ine ndiima pa kasupe wa madzi, ndipo pakhale, kuti namwali amene atuluka kudzatunga madzi ndimwe pang'ono m'mtsuko mwako;


Pereka njira yako kwa Yehova; khulupiriranso Iye, adzachichita.


Ndipo wansembe wa Midiyani anali nao ana aakazi asanu ndi awiri, amene anadza kudzatunga madzi; ndipo anadzaza mimwero kuti amwetse gulu la atate wao.


umlemekeze m'njira zako zonse, ndipo Iye adzaongola mayendedwe ako.


Kunali ngati ora lachisanu ndi chimodzi. Kunadza mkazi wotuluka mu Samariya kudzatunga madzi. Yesu ananena naye, Undipatse Ine ndimwe.


Posamveka phokoso la amauta potunga madzi, pomwepo adzafotokozera zolungama anazichita Yehova, zolungama anazichita m'madera ake, mu Israele. Pamenepo anthu a Yehova anatsikira kuzipata.


Pakukwera kumzindako anapeza anthu aakazi alikutuluka kuti akatunge madzi, nanena nao, Mlauliyo alipo kodi?


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa