Genesis 23:8 - Buku Lopatulika8 Ndipo ananena nao, kuti, Ngati mukandivomereza kuti ndiike wakufa wanga ndisamthirenso maso, mundimvere ine, mundinenere ine kwa Efuroni mwana wake wa Zohari, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ndipo ananena nao, kuti, Ngati mukandivomereza kuti ndiike wakufa wanga ndisamthirenso maso, mundimvere ine, mundinenere ine kwa Efuroni mwana wake wa Zohari, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 naŵauza kuti, “Ngati mukuvomera kuti ndiike mkazi wangayu kuno, chonde pemphereni Efuroni Muhiti, mwana wa Zohari, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 nati, “Ngati mwaloladi kuti ndiyike mkazi wanga kuno, ndiye ndimvereni. Mundipemphere kwa Efroni mwana wa Zohari Onani mutuwo |