Genesis 23:7 - Buku Lopatulika7 Ndipo anauka Abrahamu naweramira anthu a m'dzikomo, ana a Hiti. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Ndipo anauka Abrahamu naweramira anthu a m'dzikomo, ana a Hiti. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Apo Abrahamu adaimirira nkuŵeramira anthuwo, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Tsono Abrahamu anayimirira naweramira anthu a dziko la Hiti aja Onani mutuwo |