Genesis 23:3 - Buku Lopatulika3 Ndipo Abrahamu anauka pa wakufa wake, nanena kwa ana a Hiti, nati, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndipo Abrahamu anauka pa wakufa wake, nanena kwa ana a Hiti, nati, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Kenaka adasiya mtembo wa mkazi wakewo, nakalankhula ndi anthu a ku Hiti kuti, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Kenaka Abrahamu ananyamuka pamene panali mtembo wa mkazi wakepo kupita kukayankhula ndi anthu a ku Hiti. Ndipo anati, Onani mutuwo |