Genesis 23:17 - Buku Lopatulika17 Ndipo munda wa Efuroni umene unali mu Makipela, umene unali patsogolo pa Mamure, munda ndi phanga lili momwemo, ndi mitengo yonse inali m'mundamo, yokhala m'malire monse mozungulira momwemo, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Ndipo munda wa Efuroni umene unali m'Makipela, umene unali patsogolo pa Mamure, munda ndi phanga lili momwemo, ndi mitengo yonse inali m'mundamo, yokhala m'malire monse mozungulira momwemo, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Umu ndimo m'mene kadziko kaja ka Efuroni ka ku Makipera, kuvuma kwa Mamure, kadasandukira ka Abrahamu. Panali munda ndi phanga lokhala m'malire mwa mundawo, pamodzi ndi mitengo yonse yam'mundamo mpaka kukalekeza ku malire ake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Choncho munda wa Efroni wa ku Makipela umene unali kufupi ndi Mamre, kuphatikiza munda, phanga linali mʼmenemo pamodzi ndi mitengo yonse ya mʼmundamo, zinaperekedwa Onani mutuwo |