Genesis 23:12 - Buku Lopatulika12 Ndipo Abrahamu anawerama pamaso pa anthu a m'dzikomo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndipo Abrahamu anawerama pamaso pa anthu a m'dzikomo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Apo Abrahamu adaŵerama pamaso pa anthu onse aja, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Apo Abrahamu anaweramanso mwaulemu pamaso pa anthu a mʼdzikolo Onani mutuwo |