Genesis 23:11 - Buku Lopatulika11 Iai, mfumu, mundimvere ine; munda ndikupatsani inu, ndi phanga lili m'menemo ndikupatsani inu, pamaso pa ana a anthu anga ndikupatsani inu; ikani wakufa wanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Iai, mfumu, mundimvere ine; munda ndikupatsani inu, ndi phanga lili m'menemo ndikupatsani inu, pamaso pa ana a anthu anga ndikupatsani inu; ikani wakufa wanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 “Ai, mbuyanga. Ine ndikupatsani munda wonsewu pamodzi ndi phanga lomweli. Ndikupatsani chabe malowo pamaso pa anthu anga onseŵa, kuti muikemo amai amene atisiyaŵa.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 nati, “Ayi mbuye wanga tandimverani, ine ndikukupatsani mundawo ndiponso phanga limene lili mʼmenemo. Ndikukupatsani malowa pamaso pa anthu a mtundu wanga. Chonde ikani mtembo wamkazi wanu.” Onani mutuwo |