Genesis 22:6 - Buku Lopatulika6 Ndipo Abrahamu anatenga nkhuni za nsembe yopsereza, nazisenzetsa Isaki mwana wake; natenga moto m'dzanja lake ndi mpeni; nayenda pamodzi onse awiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Ndipo Abrahamu anatenga nkhuni za nsembe yopsereza, nazisenzetsa Isaki mwana wake; natenga moto m'dzanja lake ndi mpeni; nayenda pamodzi onse awiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Abrahamu adasenzetsa Isaki nkhuni zokaotchera nsembe yopsereza ija, iyeyo adaatenga moto m'manja mwake, pamodzi ndi mpeni, onse nkumayendera limodzi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Abrahamu anatenga nkhuni za nsembe yopsereza zija namusenzetsa mwana wake Isake, ndipo iye mwini anatenga moto ndi mpeni. Pamene awiriwo amayendera pamodzi, Onani mutuwo |