Genesis 22:4 - Buku Lopatulika4 Tsiku lachitatu Abrahamu anatukula maso ake naona malowo patali. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Tsiku lachitatu Abrahamu anatukula maso ake naona malowo patali. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Pa tsiku lachitatu lake Abrahamu adaona malowo chapatali. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Pa tsiku lachitatu, Abrahamu anakweza maso ake ndipo anaona malowo chapatali. Onani mutuwo |