Genesis 22:14 - Buku Lopatulika14 Ndipo Abrahamu anatcha dzina lake la malowo Yehova-Yire: monga ati lero lomwe, M'phiri la Yehova chidzaoneka. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Ndipo Abrahamu anatcha dzina lake la malowo Yehova-Yire: monga ati lero lomwe, M'phiri la Yehova chidzaoneka. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Abrahamu adaŵatcha malowo kuti Chauta adapatsa. Ndipo mpaka lero lino anthu amati, “Paphiri la Chauta adzapatsa.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Choncho Abrahamu anatcha malo amenewa kuti Yehova-Yire (Wopereka). Ndipo mpaka lero amatchula malowo kuti ndi “Pa phiri la Yehova wopereka.” Onani mutuwo |