Genesis 22:10 - Buku Lopatulika10 Ndipo Abrahamu anatambasula dzanja lake, natenga mpeni kuti amuphe mwana wake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndipo Abrahamu anatambasula dzanja lake, natenga mpeni kuti amuphe mwana wake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Tsono adasolola mpeni kuti amuphe mwana wakeyo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Kenaka Abrahamu anatambasula dzanja lake natenga mpeni kuti aphe mwana wake. Onani mutuwo |