Genesis 21:25 - Buku Lopatulika25 Ndipo Abrahamu anamdzudzula Abimeleki chifukwa cha chitsime cha madzi, anyamata ake a Abimeleki anachilanda. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Ndipo Abrahamu anamdzudzula Abimeleki chifukwa cha chitsime cha madzi, anyamata ake a Abimeleki anachilanda. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Pambuyo pake Abrahamu adamdandaulira Abimeleki za chitsime chimene antchito ake adaalanda. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Kenaka Abrahamu anadandaula kwa Abimeleki pa za chitsime chimene antchito a Abimeleki analanda. Onani mutuwo |