Genesis 21:26 - Buku Lopatulika26 Ndipo anati Abimeleki, Sindinadziwe amene anachita icho; ndipo iwe sunandiuze ine, ndiponso sindinamve koma lero lino. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 Ndipo anati Abimeleki, Sindinadziwe amene anachita icho; ndipo iwe sunandiuze ine, ndiponso sindinamve koma lero lino. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 Abimeleki adati, “Sindikudziŵa amene adachita zimenezi. Ngakhale inu nomwe simudandiwuze, ndipo ine kumva nkomweku.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 Koma Abimeleki anati, “Ine sindikudziwa amene anachita zimenezi. Iwe sunandiwuze, ndipo ndazimva lero zimenezi.” Onani mutuwo |