Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 20:8 - Buku Lopatulika

8 Ndipo Abimeleki analawira m'mamawa, naitana anyamata ake onse, nanena zonse zimenezo m'makutu mwao, ndipo anthu anaopa kwambiri

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 Ndipo Abimeleki analawira m'mamawa, naitana anyamata ake onse, nanena zonse zimenezo m'makutu mwao, ndipo anthu anaopa kwambiri

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 M'maŵa mwake, m'mamaŵa, Abimeleki adaitana antchito ake onse naŵauza zonsezi, ndipo anthuwo adachita mantha kwambiri.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 Mmamawa mwake Abimeleki anayitanitsa akuluakulu ake onse, ndipo atawafotokozera zimene zinachitika, iwo aja anachita mantha kwambiri.

Onani mutuwo Koperani




Genesis 20:8
2 Mawu Ofanana  

Tsopano, umbwezere munthuyo mkazi wake; chifukwa iye ndiye mneneri, ndipo adzakupempherera iwe, ndipo udzakhala ndi moyo: koma ukaleka kumbwezera, udziwe kuti udzafa ndithu, iwe ndi onse amene uli nao.


Ndipo Abimeleki anaitana Abrahamu, nati kwa iye, Watichitira ife chiyani iwe? Ndakuchimwiranji iwe kuti waufikitsa pa ine ndi pa ufumu wanga uchimo waukulu? Wandichitira ine zosayenera kuzichita.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa