Genesis 20:5 - Buku Lopatulika5 Kodi iye sanati kwa ine, Ndiye mlongo wanga: ndipo mkazi iye yekha anati, Iye ndiye mlongo wanga: ndi mtima wanga wangwiro ndi manja anga osachimwa ndachita ine ichi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Kodi iye sanati kwa ine, Ndiye mlongo wanga: ndipo mkazi iye yekha anati, Iye ndiye mlongo wanga: ndi mtima wanga wangwiro ndi manja anga osachimwa ndachita ine ichi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Abrahamu pondiwuza adati, ‘Ndi mlongo wanga,’ ndipo iyenso mwini wake ankanena kuti, ‘Ndi mlongo wanga.’ Ine pochita zimenezi, mtima wanga sudanditsutse konse, ndipo sindidalakwe.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Kodi Abrahamu sanandiwuze kuti iyeyu ndi mlongo wake? Ndiponso mkaziyu ankanena kuti Abrahamu ndi mlongo wake. Choncho ine pochita izi, ndinkachita moona mtima ndiponso mopanda chinyengo.” Onani mutuwo |