Genesis 20:12 - Buku Lopatulika12 Koma ndiye mlongo wanga ndithu, mwana wa atate wanga, koma si mwana wa amai wanga: ndipo anakhala ndi ine mkazi wanga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Koma ndiye mlongo wanga ndithu, mwana wa atate wanga, koma si mwana wa amai wanga: ndipo anakhala ndi ine mkazi wanga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Komabetu, kunena zoona, ndi mlongo wangadi ameneyu, chifukwa ndi mwana wa bambo wanga, koma osati womubala mai wanga, ineyo nkumukwatira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Komabe kunena zoona, iyeyu ndi mlongo wangadi, mwana wamkazi wa abambo anga ngakhale kuti si ife a mayi mmodzi. Tsono akhoza kukhala mkazi wanga. Onani mutuwo |