Genesis 20:1 - Buku Lopatulika1 Abrahamu ndipo anachoka kumeneko kunka ku dziko la kumwera, ndipo anakhala pakati pa Kadesi ndi Suri, ndipo anakhala ngati mlendo mu Gerari. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Abrahamu ndipo anachoka kumeneko kunka ku dziko la kumwera, ndipo anakhala pakati pa Kadesi ndi Suri, ndipo anakhala ngati mlendo m'Gerari. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Abrahamu adachokako ku Mamure kuja napita ku Negebu, chigawo chakumwera. Adakakhala pakati pa mzinda wa Kadesi ndi dziko la Suri, nakhazikika ku dziko la Gerari. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Abrahamu anachokako kumeneko napita ku Negevi ndipo anakakhala ku dziko la Gerari, limene lili pakati pa mzinda wa Kadesi ndi mzinda wa Suri. Anakhala ku Gerari kwa kanthawi, Onani mutuwo |