Genesis 2:13 - Buku Lopatulika13 Dzina la mtsinje wachiwiri ndi Gihoni: umenewo ndiwo wozungulira dziko lonse la Kusi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Dzina la mtsinje wachiwiri ndi Gihoni: umenewo ndiwo wozungulira dziko lonse la Kusi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Mtsinje wachiŵiri ndi Gihoni, ndipo umayenda mozungulira dziko la Kusi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Dzina la mtsinje wachiwiri ndi Gihoni; uwu umazungulira dziko lonse la Kusi. Onani mutuwo |