Genesis 19:6 - Buku Lopatulika6 Ndipo Loti anatulukira kwa iwo pakhomo, natseka chambuyo pakhomo pake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Ndipo Loti anatulukira kwa iwo pakhomo, natseka chambuyo pakhomo pake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Loti adatuluka panja natseka chitseko. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Loti anatuluka panja kukakumana nawo natseka chitseko Onani mutuwo |