Genesis 19:32 - Buku Lopatulika32 tiyeni, timwetse atate vinyo, tidzagona naye, kuti tisunge mbeu za atate wathu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201432 tiyeni, timwetse atate vinyo, tidzagona naye, kuti tisunge mbeu za atate wathu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa32 Tiye tiŵaledzeretse abamboŵa kuti agone nafe, kuti mtundu usathe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero32 Tiye tiwamwetse vinyo ndipo tigone nawo. Tikatero mtundu wathu udzakhalapobe.” Onani mutuwo |