Genesis 19:12 - Buku Lopatulika12 Ndipo anthu aja anati kwa Loti, Kodi muli nao ena pano? Mkamwini, ndi ana ako aamuna, ndi ana ako aakazi, ndi onse ali nao m'mzinda muno, utuluke nao m'malo muno: Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndipo anthu aja anati kwa Loti, Kodi muli nao ena pano? Mkamwini, ndi ana ako amuna, ndi ana ako akazi, ndi onse ali nao m'mudzi muno, utuluke nao m'malo muno: Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Anthu aŵiriwo adafunsa Loti kuti, “Kodi aliponso wina aliyense amene uli naye kuno? Tenga ana ako aamuna, ana ako aakazi, akamwini ako ndi wina aliyense wachibale amene ali mumzinda muno, mutuluke, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Anthu awiri aja anati kwa Loti, “Kodi uli ndi wina aliyense pano, kaya ndi akamwini ako, kaya ndi ana ako aamuna kapena aakazi, kapena aliyense mu mzindamu amene ndi anzako? Atulutse onse muno, Onani mutuwo |