Genesis 19:11 - Buku Lopatulika11 Ndipo anachititsa khungu m'maso mwa anthu amene anali pakhomo pa nyumba, aang'ono ndi aakulu, ndipo anavutika kufufuza pakhomo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Ndipo anachititsa khungu m'maso mwa anthu amene anali pakhomo pa nyumba, ang'ono ndi akulu, ndipo anavutika kufufuza pakhomo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Kenaka adaŵachititsa khungu anthu onse amene adaaima pabwalowo, achinyamata ndi okalamba omwe, kotero kuti sadathenso kuwona khomo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Kenaka anawachititsa khungu anthu amene anali panja pa nyumba aja, aangʼono ndi aakulu omwe, kuti asaone pa khomo. Onani mutuwo |