Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 19:10 - Buku Lopatulika

10 Koma anthu aja anatulutsa dzanja lao, namlowetsa Loti momwe anali iwo m'nyumba, natseka pakhomo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

10 Koma anthu aja anatulutsa dzanja lao, namlowetsa Loti momwe anali iwo m'nyumba, natseka pakhomo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

10 Koma anthu aŵiri anali m'kati aja adamkokera Lotiyo m'nyumba, natseka chitseko.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

10 Koma anthu aja anali mʼkatiwa anasuzumira namukokera Loti uja mʼkati mwa nyumba nʼkutseka chitseko.

Onani mutuwo Koperani




Genesis 19:10
2 Mawu Ofanana  

Ndipo anadza ku Sodomu madzulo amithenga awiri; ndipo Loti anakhala pa chipata cha Sodomu, ndipo Loti anaona iwo, nauka kuti akakomane nao, ndipo anaweramitsa pansi nkhope yake.


Ndipo anachititsa khungu m'maso mwa anthu amene anali pakhomo pa nyumba, aang'ono ndi aakulu, ndipo anavutika kufufuza pakhomo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa