Genesis 18:7 - Buku Lopatulika7 Ndipo Abrahamu anafulumira kunka kuzoweta, natenga kamwana ka ng'ombe kofewa ndi kabwino, napatsa mnyamata, ndipo anafulumira kuphika. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Ndipo Abrahamu anafulumira kunka kuzoweta, natenga kamwana ka ng'ombe kofewa ndi kabwino, napatsa mnyamata, ndipo anafulumira kuphika. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Pamenepo Abrahamu adathamanga nakatenga mwanawang'ombe wonenepa, nampereka kwa wantchito kuti akonze mwamsanga. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Kenaka Abrahamu anakatenga mwana wangʼombe wonenepa ndi wofewa bwino ndi kupatsa wantchito wake amene anachita changu kukonza ndiwoyo. Onani mutuwo |