Genesis 18:3 - Buku Lopatulika3 Mbuyanga, ngatitu ndi ndikapeza ufulu pamaso panu, musapitiriretu pa kapolo wanu; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Mbuyanga, ngatitu ndi ndikapeza ufulu pamaso panu, musapitiriretu pa kapolo wanu; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 nati, “Mbuyanga, ngati ndapeza kuyanja pamaso panu, chonde musapitirire pakhomo pa mtumiki wanu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 “Ngati mwandikomera mtima, mbuye wanga, musamulambalale mtumiki wanu. Onani mutuwo |