Genesis 17:21 - Buku Lopatulika21 Koma pangano langa ndidzalimbikitsa ndi Isaki, amene Sara adzakubalira iwe nthawi yomwe ino chaka chamawa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Koma pangano langa ndidzalimbikitsa ndi Isaki, amene Sara adzakubalira iwe nthawi yomwe yino chaka chamawa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Koma ndidzasunga chipangano changa ndi mwana wako Isaki amene adzabadwa mwa Sara pa nyengo yonga yomwe ino chaka chamaŵachi.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Koma ndidzasunga pangano langali ndi Isake amene Sara adzakubalira pofika nthawi ngati ino chaka chamawa.” Onani mutuwo |