Genesis 17:15 - Buku Lopatulika15 Ndipo Mulungu anati kwa Abrahamu, Koma Sarai mkazi wako, usamutcha dzina lake Sarai, koma dzina lake ndi Sara. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Ndipo Mulungu anati kwa Abrahamu, Koma Sarai mkazi wako, usam'tcha dzina lake Sarai, koma dzina lake ndi Sara. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Pambuyo pake Mulungu adauza Abrahamu kuti, “Mkazi wakoyu usamutchulenso kuti Sarai. Tsopano dzina lake ndi Sara. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Mulungu anatinso kwa Abrahamu, “Sarai mkazi wako, sudzamutchanso Sarai; dzina lake lidzakhala Sara. Onani mutuwo |